Timu ya Malawi ya mpira wa miyendo ya atsikana lero yafanso kachiwiri 2-1 ndi timu ya South Africa mu masewelo a pa ubale omwe anachitikira pa bwalo la Lucas Moripe m'dziko la South Africa. Chigawo choyamba chinatha chetechete ndipo chigawo chachiwiri chitayamba mphindi zochepa chabe Malawi inapata mwayi wa kona yomwe anasema Ireen Khumalo kukapeza […]
The post Kubwezera nkhonya kwakanika, South Africa yapamanthanso Scorchers kachiwiri appeared first on Malawi 24.