Wapampando wamsonkhano waukulu wa chipani cha Malawi Congress (MCP), a Kezzie Msukwa watsimikizira atolankhani kum'mawaku ku Lilongwe kuti ganizo la chipanichi loletsa aliyese kuima pamipando yemwe wangolowa kumene ndipo sadathe zaka ziwiri likadalipo. A Msukwa anenetsa kuti izi zili motere pofuna kusunga umwini wa chipani. Iwo anenetsa kuti kwina kulikonse kumakhala ndondomeko zosankhira adindo ake […]
The post Konveshoni ya MCP yapsa pa 10 August: Koma anenetsa kuti obwera kumene muchipani sakapisana nawo appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.