Pomwe namondwe otchedwa Jude wayandikira kulowa m'dziko muno kuchoka ku gombe la Nampula m'dziko la Mozambique, a Malawi amene tikukhala m'madera okhudzidwa maka mchigawo chakum'mwera, tiyeni tikhale osamala chifukwa pamapeto pa zonsezi, pali chiyembekezo kuti zonse zikhala bwino. Anthu amene tikukhala m'phepete mwa mitsinje, tiyeni tisamuke ndikukakhala m'malo omwe ndi otetezedwa ku namondweyu. Nkutheka timaolokanso […]
The post Khalani atcheru, zitetezeni ku namondwe otchedwa Jude appeared first on Malawi 24.