Wachiwiri kwa wapampando wa gulu lowona za Covid19, a Wilfred Chalamira Nkhoma, ati katemera 210,000 akhala atatha mphamvu pakutha kwa chakachi. Iwo amayankhula izi pa msonkhano omwe bungwe la madotolo linakonza kudzera pa njira ya Zoom. Iwo anati katemera ali ndi nthawi yochepa ndipo amatha mphamvu mwamsanga. Izo ndizo zinawakakamiza kuyamba njira yopita khomo ndi […]
The post Katemera 210,000 wa Covid atha mphamvu pakutha kwa chakachi appeared first on Malawi 24.