Bungwe la Centre for Democracy and Economic Development Initiatives (CDEDI) lati m’chitidwe wakatangale ku nthambi yogura ndi kugulitsa katundu wa boma ya Public and Disposal of Assets Authority (PPDA) wamanga nthenje ndipo Boma likuyenera kuwunika komanso kuthetsa m’chitidwewu madzi asanafike m’khosi. Mkulu wa bungweli, Sylvester Namiwa, wanena izi lero pa msonkhano wa atolankhani omwe unachitikira […]
The post Katangale wachuluka ku nthambi yogura ndi kugulitsa katundu wa boma - Cdedi appeared first on Malawi 24.