Kampani ya FINCA yomwe ikusangalala kuti yatha zaka makumi atatu (30) ikugwira ntchito za za chuma m'dziko muno, yati ndi bodza lankunkhuniza kuti imalanda makasitomala ake katundu zikawavuta pobweza ngongole. Izi ndi malingana ndi mkulu wa kampaniyi a Charles Bello omwe anena izi Lolemba pa 5 August 2024 pakutha pamwambo wosangalalira zaka 30 zomwe kampaniyi […]
The post Kasitomala zikamuvuta timakambirana – FINCA appeared first on Malawi 24.