Pomwe phungu wa nyumba ya malamulo ku m’mawa kwa boma la Rumphi a Kamlepo Kalua watulutsidwa pa belo lero, apolisi amangaso m'busa wa mpingo wa CCAP pamlandu okhudza kufalitsa za ngozi ya ndege yomwe inapha wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima ndi anthu asanu ndi atatu. Wofalitsa nkhani za apolisi m’dziko muno […]
The post Kamlepo watuluka pa belo, m’busa wina wamangidwaso appeared first on Malawi 24.