'Khaaa kuti khaaa..'Julius Mithi apata shuwa pomwe ma loya odziwika bwino mdziko muno a Silvester Ayuba James ndi a Khwima Mchizi ati akayimilira mwa ulele a Mithi omwe awamanga dzulo mu mzinda wa Mzuzu. A Ayuba James omwe alemba nkhani yokhudza kuyimila a Mithi mwaulele pa tsamba lawo la mchezo la Facebook, pomwe anapita kukacheza […]
The post Julius Mithi apata shuwa appeared first on Malawi 24.