Katswiri womwetsa zigoli mu timu ya dziko lino Flames, Gabadinho Mhango, watengera timu yake ya Marumo Gallants ku khothi pomwe akufuna ndalama zoposa K82 miliyoni kwacha kamba kogwiritsa ntchito zithuzi zake. Malingana ndi tsamba la Soccer Betting News la m’dziko la South Africa, Mhango akuloza chala timu ya Marumo Gallants kuti yakhala ikugwiritsa ntchito zithuzi […]
The post Gaba wasumira timu yake, akufuna K82 miliyoni appeared first on Malawi 24.