Timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino ya the Flames yanyamuka ulendo wokakumana ndi Tunisia m'masewelo olimbirana malo ku mpikisano wa 2026 FIFA World Cup kudzera pa bwalo la ndenge la Kamuzu international mu nzinda wa Lilongwe, pomwe yanyamuka opanda Frank Gabadinho Mhango ndi otseka kumbuyo Charles Petro omwe ndi ovulala. Pa ulendo wake […]
The post Gaba ndi Petro atsala pomwe Flames yanyamuka wa ku Tunisia appeared first on Malawi 24.