Fomo yaluza womwetamweta pamene yalepherana ndi anyamata a Mighty Tigers. Fomo inapeza chigoli choyamba pa mphindi khumi ndi imodzi kudzera mwa osewera Hassan Hussein. Pamene zimakwana mphindi makumi awiri ndi ziwiri (22) naye osewera wa timuyi Hassan Luwemba anagoletsanso chigoli cha nambala 2 zomwe zinapangitsa timu ya Fomo kutsogola ndi zigoli ziwiri kwa duu. Mphindi […]
The post Fomo yaluza womwetamweta appeared first on Malawi 24.