Bungwe loyendetsa mpira wa miyendo la Football Association of Malawi (FAM), motsogozedwa ndi mtsogoleri wake a Fleetwood Haiya, lavomeleza chigawo cha ku m'mawa kukhala imodzi mwa zigawo zake. Izi zikutanthauza kuti zigawozi zawonjezereka kufika pa khumi (10) ndipo anthu omwe adzivotera mtsogoleri wa bungweli awonjezerekanso mwa zina. Ma boma a chigawo chatsopanochi akuphatikiza ma boma […]
The post Fleetwood Haiya ndi masomphenya ake, FAM ikusintha appeared first on Malawi 24.