Bungwe lowona masewelo a mpira wa miyendo pa dziko lonse la FIFA lasankha a Godfrey Nkhakananga kuti akayimbile masewelo a ndime ya chipulula a mu mpikisano wa World Cup a mchaka cha 2026. Malingana ndi FIFA, Nkhakananga adzayimbila masewelo a pakati pa Sierra Leone ndi Djibouti omwe adzachitike pa 5 June 2024 pa bwalo la […]
The post FIFA yawona oyimbila Nkhakananga appeared first on Malawi 24.