Nkhani ndi ka Mnyamata, fisi adakana mtsatsi, bungwe loyendetsa za mpira wa miyendo mu dziko muno lakana Condom. Malipoti anatchuka kuti bungweli, la FAM, likufufuza mphunzitsi wina oti mwina ndikukatenga timu ya Flames ku chikho cha mu Africa. Malinga ndi malipotiwa, ati a FAM akhumudwa ndi mmene timu ya fuko, ya Flames, yachitila mu mipikisano […]
The post FAM yakana Condom appeared first on Malawi 24.