Pomwe chiwerengero cha anthu omwe akupezeka ndikachilombo ka corona chayambilaso kukwera, boma labwezeretsa zina mwaziletso zomwe pakatipa zinasiya kugwira ntchito. Izi zadziwika lachitatu masana pomwe nduna yazaumoyo a Khumbize Kandodo Chiponda omweso ndi mmodzi mwa akuluakulu akomiti yamtsogoleri wa dziko yoyang'anira ntchito yolimbana ndi mlili wa covid-19, amayankhula pansonkhano wa atolonkhani ku Lilongwe. Malingana ndi […]
The post Coronavirus: Boma labwezeretsa ziletso appeared first on Malawi 24.