Chiwerengero cha anthu omwe akumwalira ndi kachirombo ka corona chikunka chikukwelerabe pomwe m’maola 24 apitawa anthu 25 ndi omwe atisiya atadwala matendawa. Izi ndimalingana ndi nduna yazaumoyo a Khumbize Kandodo Chiponda omweso ndi wapampando wakomiti yamtsogoleri wa dziko yoyang'anira ntchito yothana ndi mlili wa covid-19. A Kandodo Chiponda omwe amayankhula Lachinayi madzulo pomwe amalidziwitsa dziko […]
The post Coronavirus: anthu 25 amwalira m’maola 24 apitawa appeared first on Malawi 24.