Timu ya mpira wa miyendo ya Malawi the Flames' yaswa timu ya South Africa ndi chigoli chimodzi kwa duu pa bwalo la Bingu mu mzinda wa Lilongwe. Masewelo a mu gawo lachiwiri (Round 2 ) ya African Nations Championship CHAN Malawi yamwemwetera mu chigoli chochoka kwa Zeliet Nkhoma pa mphindi ya 87. Kalisto Pasuwa anadalira […]
The post Chimwemwe mtsaya, Flames yapantha South Africa appeared first on Malawi 24.