Galimoto ya boma yomwe amayendera mkulu wa za malamulo mu boma a Thabo Chakaka Nyirenda yaswedwa dzulo mu Lilongwe. Malinga ndi malipoti, bambo wina wokwiya dzulo usiku anatengera yekha malamulo m'manja ndi kuswa galimoto loyendera bambo Chakaka ati chifukwa akhala akusokoneza banja lake. Bamboyu, a Harris Nantikwa, analemba pa tsamba lawo la mchezo la Facebook […]
The post Chakaka chisembwere ku boma: wamkulu wa boma aphwanyiridwa galimoto kopakula appeared first on Malawi 24.