Atakhala kwa kanthawi osatulutsa mawu oyikira kumbuyo utsogoleri omwe ulipowu mwachindunji komanso tsogolo la chomwe akufuna, wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Michael Usi lero abwera poyera kuwatsimikizira anthu za ubwino waboma ndi utsogoleri omwe ulipo pano wa a Lazarus Chakwera. A Usi Alankhula lero ku Mwanza komwe anakumana ndi anthu komanso mafumu powamemeza […]
The post Boma ndi Lomweli - Usi appeared first on Malawi 24.