Boma kudzera kuunduna wazachitetezo cha mdziko lalengeza kuti kuyambira Lachiwiri sabata yamawa likhala likubweza njinga zamoto zonse zomwe linalanda. Izi ndimalinga ndi nduna ya za chitetezo chamdziko a Richard Chimwendo Banda omwe amayankhula kunyumba yamalamulo Lachinayi pa 8 june, 2021. A Chimwendo Banda anati boma lapanga chiganizochi polingalira kufunika kwanjingazi pankhani za mayendedwe mdziko muno […]
The post Boma libweza njinga zamoto zomwe linalanda appeared first on Malawi 24.