Boma la Rwanda lati latseka makachisi oposera 4,000 ati kaamba kopemphelera mu malo a umve komanso kugwilitsa ntchito zimkuza mawu zomwe zimachita phokoso losaneneka. Malingana ndi malipoti a nyumba yofalitsa nkhani ya BBC, zipembedzo zomwe zakhuzidwa ndi za chi pentekositi komanso chisilamu. Nduna yowona za maboma ang'ono m'dziko la Rwanda, Jean Claude Musabyimana wati boma […]
The post Boma la Rwanda litseka kachisi oposera 4,000 appeared first on Malawi 24.