Anthu okhala mu mzinda wa Blantyre ayembekezere kuti chaka cha mawa mtengo wa madzi utha kukweraso kaamba koti bungwe logulitsa madzi la Blantyre Water Board (BWB) lati likufuna kupempha boma kuti likwezeso mtengo wa madziwu ndi K40 pa K100 iliyonse. Izi zadziwika pamkumano omwe bungweli linali nawo sabata ino mumzinda wa Blantyre komwe mwazina limakhazikitsa […]
The post Blantyre Water Board ikufuna kukwezaso mtengo wa madzi chaka cha mawa appeared first on Malawi 24.