M'tsogoleri wotsutsa boma ku Nyumba ya Malamulo George Chaponda, wati bilu yomwe imafuna kupita ku Nyumba ya Malamulo yoletsa munthu yemwe wafika zaka 80 kuyimira pa udindo wa m'tsogoleri wa dziko lino sipitanso ku nyumbaku. A Chaponda atsimikiza za izi pa tsamba lawo la mchezo atamaliza mkumano wa business committee omwe umachitikira ku nyumba ya […]
The post Bilu ya zaka sipitanso ku Nyumba ya Malamulo - Chaponda appeared first on Malawi 24.