Nyumba yosindikiza nkhani ya m’dziko la United Kingdom ya British Broadcasting Company (BBC), yawonjezera mkwiyo komaso chisoni cha a Malawi pomwe yanena kuti malemu Saulos Chilima anazengedwapo milandu ya katangale m'boma. Lachiwiri, BBC Africa yatulutsa nkhani momwe ikukamba za moyo wa wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino malemu Chilima omwe afa pamodzi ndi anthu ena […]
The post BBC Itipepese - aMalawi appeared first on Malawi 24.