Apolisi ku Makokola m’boma la Mangochi amanga bambo wa zaka 35 zakubadwa, James Phiri pomuganizira kuti anagonana ndi ana awiri omwe ndi pachibale azaka 12 komanso 10. Malingana ndi mneneri wa polisi ya Mangochi, Amina Tepani Daudi, anawa amagulitsa samosa pa msika wa pa Makawa pomwe Phiri, yemwe amakonda kugulagula samosa'yu, adagula samosa muwiri ndikuwapatsa […]
The post Bambo anjatidwa kamba kogwililira ana awiri pa tchalitchi appeared first on Malawi 24.