Woyankhulapo pankhani zochitika m'dziko, a George Chaima, apempha a polisi kuti athane ndi aliyense opezeka akulemba makalata a bodza okhudza andale komanso anthu ena. Iwo alankhula izi pomwe a polisi akhazikitsa kafukufuku ofuna kupeza anthu omwe anatulutsa kalata yabodza yofotokoza zakutula pansi udindo kwa mtsogoleri wachiwiri wa dziko lino a Saulos Klaus Chilima. A Chaima […]
The post Apolisi awapempha kuti athane ndi omwe amatulutsa makalata abodza appeared first on Malawi24.