Mayi wa zaka 26, Lusayo Kaliza, ali m'manja mwa a polisi ku Lilongwe kamba koganidzilidwa kuti anaba mankhwala ndi zipangizo zina zogwiritsila ntchito pa chipatala cha Bwaila. Iwo amachokera m'mudzi mwa Mchochoma mfumu yayikulu Kamenyagwaza ku Dedza. Malingana ndi m'neneri wa a polisi ku Lilongwe Sub Inspector Hastings Chigalu, mayiyu amagwira ntchito pa chipatala cha […]
The post Apolisi amanga ogwira ntchito pa chipatala kamba kokuba mankhwala appeared first on Malawi 24.