M’modzi mwa anthu omwe amayankhulapo pankhani zokhudza chitetezo cha mdziko a Sherrif Kaisi adzudzula apolisi kaamba komanga omenyera ufulu a Sylvester Namiwa mwankhanza. A Namiwa amangidwa Lachitatu pomwe amatsogolera zionetsero zomwe cholinga chaka chinali kufuna kuti akuluakulu a nyumba yamalamulo komaso mtsogoleri wa dziko lino achitepo kanthu pa kuzembetsedwa kwa bilu yokhudza ngongole. Malingana ndi […]
The post Apolisi adzudzulidwa pomanga a Namiwa mwankhanza appeared first on Malawi 24.