Kwanu kwanu m'thengo mudalaka njoka. N'kutheka a malume kapena azakhali adatchona mu dziko la Amereka lija ndi kuwaona tsopano. Tsache limene anyamula bambo Trump lokonza mu dziko la Amereka likhudza mzika zina za dziko lino zimene tsopano zili pa mzere kudikila kukwera ndege kumabwelera. Malipoti ochokera mu dziko la Amereka asonyeza kuti a Malawi okwana […]
The post Anthu 56 akubwela kuno kumudzi atapitikitsidwa ndi Trump ku Amereka appeared first on Malawi 24.