Abambo awiri omwe ndi akabwerebwere a ku ndende akwidzingidwa ndi apolisi powaganizila kuti amaba katundu osiyanasiyana m’ma nyumba aanthu m’boma la Kasungu. Malingana ndi wachiwiri kwa m‘neneri wa polisi ya Kasungu, Miracle Hauli, abambowa ndi a Eleson Nkhoma azaka 25 ndi a Thomas Mwale azaka 30 ndipo anagwirapo ukayidi m’mbuyomu. A Hauli ati abambowa awapeza […]
The post Anjatidwa kamba ka umbava appeared first on Malawi 24.