Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Michael Usi ati iwo sanachoke mu chipani cha UTM koma anangothamangitsidwa. “Ndati ndikonze malo amodzi. Ku UTM sinachokeko koma anangondithamangitsako ndipo anthu ache ali pompano. Sikuti ndikudana nawo ayi, koma chilungamo chidzidziwika,” anafotokoza a Usi. Iwo anatsindikanso: “Ndimati ndikonze chifukwa anthu mumalemba kuti ayi anachokako koma ine ndinathamangitsidwa.” […]
The post Anandithamangitsa mu chipani cha UTM - Usi appeared first on Malawi 24.