Ana ongoyendeyenda (street kids) asumila m'modzi mwa oyimilira milandu Sylvester Ayuba James pa zomwe analemba pa tsamba lake la mchezo zokhudza anawa. Pa 14 January, 2025, a James analemba pa tsamba lake la mchezo kupempha Boma kuti liziwombera ana omwe amavutitsa anthu maka kuwabera mu mzinda wa Lilongwe. Mukalata yawo yomwe alemba kudzera mwa omwe […]
The post Ana ongoyendeyenda asumila Ayuba James pa zomwe analemba pa tsamba lake la mchezo appeared first on Malawi 24.