Phungu wa dela la Zomba Malosa, Grace Kwelepeta walimbikitsa amayi kuti akhale patsogolo kuyamika komanso kupemphelera dziko maka pamene dziko la Malawi likuyandikira kupita ku masankho ponena kuti mapemphelo ndi omwe amabweletsa umodzi ndi kupeleka atsogoleri oyenera komanso kupulumutsa dziko ku zophinja. A Kwelepeta anayankhula izi pomwe anakhala nawo pa mwambo wa mapemphero wa amayi […]
The post Amayi akhale patsogolo kupemphelera dziko, zisankho - Kwelepeta appeared first on Malawi 24.