Apolisi kwa Bvumbwe m'boma la Thyolo amanga abambo anayi powaganizira kuti amafuna kuzembetsa anthu okwana 65. Malingana ndi ofalitsa nkhani pa polisi ya Limbe, Aubrey Singanyama, m’modzi mwa anayi oganizilidwawa ndi a Maxwell Banda a zaka 32 omwe amangidwa pamodzi ndi anzawo ena atatu Lolemba sabata ino. Singanyama wati anayiwa anapita m’midzi ina m’bomali ndi […]
The post Amangidwa pofuna kuzembetsa anthu appeared first on Malawi 24.