Mkulu wa bungwe lolimbana ndi kuthana ndi mchitidwe wa ziphuphu komanso katangale la Anti-corruption Bureau, mai Martha Chizuma, ati ndi kofunika kugwirana manja kuti dziko lino lipambane pa nkhondo yolimbana ndi mchitidwe oipawu. A Chizuma amayankhula izi dzulo pomwe bungwe la ACB mogwilizana ndi khonsolo ya boma la Balaka linakonza mwambo osesa komanso kuchotsa zinyalala […]
The post Aliyense atengepo mbali polimbana ndi ziphuphu ndi katangale – Chizuma appeared first on Malawi 24.