Pamene chisankho chosankha mtsogoleri wa dziko lino chatsala pang’ono kuchitika mdziko muno, ku chipani cha UTM nako kwayaka moto kaamba koti a Patricia Kaliati omwenso amadziwikanso ndi dzina loti Akweni, aonetsa chidwi chopikisana nawo pa mpando wa mtsogoleri wa chipani chi. A Kaliati omwe ndi mlembi wamkuku wa UTM, ati iwo akhala ochilimika ku chipanichi […]
The post Akweni aonetsa chidwi chopikisana nawo paudindo wa mtsogoleri wa UTM appeared first on Malawi 24.