Mtsogoleri wachipani cha Alliance for Democracy (AFORD), Enock Chihana wati satekeseka ngakhale kuti anthu ena akukonza chiwembu chofuna kuchotsa moyo wawo komanso ena ochita nawo ndale. Chihana wayankhula izi pomwe anthu ena omwe sakudziwika agenda m'dipiti wa galimoto zomwe iye pamodzi ndi akuluakulu ena achipanichi adakwera lero Lachinayi. Malinga ndi kanema wina yemwe anthu akugawana […]
The post Akufuna ndithu wina aphedwenso – watelo Chihana appeared first on Malawi 24.