A Matthews Mtumbuka, omwe alinawo m'gulu lofuna kudzapikisana nawo pa mpando wa utsogoleri kuchipani cha United Transformation (UTM) ati ali ndi malingaliro ofuna kudzayambitsa zoti achinyamata pamodzi ndi amayi azidzakhala ndi mipando yawo yapadera ku nyumba yamalamulo. Iwo amayankhula izi kusukulu yaukachenjede ya Mzuzu pamwambo wamgonelo omwe sukuluyi idakonza pofuna kupeza ndalama zochitira mwambo wa […]
The post Achinyamata adzikhala ndi mipando ya padera ku nyumba ya Malamulo - Mtumbuka appeared first on Malawi 24.