Patangodutsa masiku ochepa abusa a Church of Central Africa Presbyterian (CCAP) Blantyre Synod atayendera mtsogoleri wakale wa dziko lino a Peter Mutharika kenako ndi kuyitanidwa kuti apalamula, nawo abusa oposa 50 a Nkhoma Synod ayendera ndi kupemphera ndi mtsogoleri wakaleyu ku nyumba kwawo ku Mangochi lero. Pa mapempherowa a Mutharika anati iwo amakhulupilira mphamvu ya […]
The post Abusa a CCAP Nkhoma Synod apempheleranso Mutharika appeared first on Malawi 24.