M’modzi wa akuluakulu a chipani cha DPP a Shadric Namalomba ati mtsogoleri wa zipani zotsutsa boma Kondwani Nankhumwa sangakawanitse chipanichi ku chisankho cha 2025 ndi chifukwa chake iwo akufuna mtsogoleri wakale wa dziko lino a Peter Mutharika kuti akayimire DPP ndi cholinga choti chipanichi chilowenso m’boma. A Nankhumwa anawonetsa chidwi chozapikisana ndi a Mutharika pa […]
The post A Nankhumwa sangakatiwinitse ku chisankho za 2025, atero a Namalomba appeared first on Malawi 24.