Mipingo yosiyanasiyana motsogodzedwa ndi mpingo wa Katolika Lachinayi yachita ziwonetsero zodana ndimaukwati amuna komanso akazi okhaokha (mathanyula) mu mzinda wa Zomba. Ku zionetserozi kudafika anthu ambiri ndipo zidayambira pa bwalo la Zomba kudzera ku St Charles Lwanga mpaka kukafika kuma office a Bwana Mkubwa (DC) wa Boma la Zomba komwe adakapereka chikalata chamadandaulo awo. Poyankhula […]
The post Mipingo ku Zomba yachita ziwonetsero zodana ndimathanyula appeared first on Malawi24.